Yesaya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tulukani mʼBabulo!+ Thawani mʼmanja mwa Akasidi. Lengezani zimenezi mofuula komanso mosangalala. Uzani anthu zimenezi.+ Zineneni kuti anthu azidziwe mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+ Yeremiya 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tulukani mʼBabulo nʼkuthawa,Ndipo pulumutsani moyo wanu.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake. Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere. Mulungu akubwezera Babulo chifukwa cha zimene anachita.+ Yeremiya 51:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Tulukani mʼBabulo anthu anga.+ Thawani mkwiyo wa Yehova+ woyaka moto kuti mupulumutse moyo wanu.+ Zekariya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Bwera Ziyoni! Thawa iwe amene ukukhala ndi mwana wamkazi wa Babulo.*+ 2 Akorinto 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Chivumbulutso 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
20 Tulukani mʼBabulo!+ Thawani mʼmanja mwa Akasidi. Lengezani zimenezi mofuula komanso mosangalala. Uzani anthu zimenezi.+ Zineneni kuti anthu azidziwe mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+
6 Tulukani mʼBabulo nʼkuthawa,Ndipo pulumutsani moyo wanu.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake. Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere. Mulungu akubwezera Babulo chifukwa cha zimene anachita.+