Yeremiya 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tulukani mʼBabulo nʼkuthawa,Ndipo pulumutsani moyo wanu.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake. Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere. Mulungu akubwezera Babulo chifukwa cha zimene anachita.+ Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.
6 Tulukani mʼBabulo nʼkuthawa,Ndipo pulumutsani moyo wanu.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake. Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere. Mulungu akubwezera Babulo chifukwa cha zimene anachita.+
11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.