Yesaya 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa tsiku limenelo, iwo adzabangulira nyamayoNgati mkokomo wa nyanja.+ Munthu aliyense amene adzayangʼane dzikolo adzaona mdima wodetsa nkhawa.Ngakhale kuwala kudzasanduka mdima chifukwa cha mitambo.+ Yoweli 2:30, 31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
30 Pa tsiku limenelo, iwo adzabangulira nyamayoNgati mkokomo wa nyanja.+ Munthu aliyense amene adzayangʼane dzikolo adzaona mdima wodetsa nkhawa.Ngakhale kuwala kudzasanduka mdima chifukwa cha mitambo.+