-
Yeremiya 50:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Inetu ndikuutsa gulu lalikulu la mitundu yamphamvu
Ndi kulibweretsa kuchokera kudziko lakumpoto kuti lidzaukire Babulo.+
Mitunduyi idzabwera ili yokonzeka kumenya nkhondo
Ndipo Babulo adzagonjetsedwa.
-