Yesaya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire,+Amene saona siliva ngati kanthuNdipo sasangalala ndi golide. Danieli 5:30, 31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.+ 31 Dariyo+ Mmedi anapatsidwa ufumuwo ndipo anali ndi zaka pafupifupi 62.
30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.+ 31 Dariyo+ Mmedi anapatsidwa ufumuwo ndipo anali ndi zaka pafupifupi 62.