-
Ezekieli 22:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Anthu amʼdzikolo abera anthu mwachinyengo komanso achita zauchifwamba.+ Iwo achitira nkhanza anthu ovutika ndi osauka. Abera mlendo mwachinyengo komanso sanamuchitire zinthu mwachilungamo.’
-