-
Yeremiya 51:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse amene akukhala mʼdziko la Kasidi
Chifukwa cha zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni inu mukuona,”+ akutero Yehova.
-