2 Mafumu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mbiri 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehoyakimu+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 25 ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu. Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+
5 Yehoyakimu+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 25 ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu. Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+