-
1 Mafumu 7:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Kenako anapanga mabeseni 10 akopa.+ Mʼbeseni lililonse munkalowa madzi okwana mitsuko 40, ndipo linali mikono 4 kuchokera mbali ina kufika mbali ina. Pa zotengera 10 zija, chilichonse chinali ndi beseni lake.
-