-
2 Mbiri 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Atatero anapanganso matcheni okhala ngati ovala mʼkhosi nʼkuwaika pamwamba pa zipilalazo ndipo anapanga makangaza* 100 nʼkuwaika kumatcheniwo.
-