-
Yeremiya 9:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 “Kodi sindikuyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” akutero Yehova.
“Kodi sindikuyenera kubwezera mtundu wa anthu oterewa?+
-
-
Yeremiya 44:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako Yehova sakanathanso kulekerera zinthu zoipa komanso zonyansa zimene munkachita ndipo dziko lanu linasanduka bwinja, chinthu chochititsa mantha ndi chotembereredwa, dziko lopanda munthu wokhalamo ngati mmene ziliri lero.+
-