Yeremiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Yehova anatambasula dzanja lake nʼkukhudza pakamwa panga.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Ndaika mawu anga mʼkamwa mwako.+
9 Kenako Yehova anatambasula dzanja lake nʼkukhudza pakamwa panga.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Ndaika mawu anga mʼkamwa mwako.+