-
Yeremiya 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kenako Yehova anandiuza kuti:
“Tsoka lidzachokera kumpoto
Ndipo lidzagwera anthu onse okhala mʼdzikoli.+
-
-
Yeremiya 10:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Tamvetserani, mdani akubwera!
-