-
Yeremiya 4:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Nenani zimenezi kwa anthu a mitundu ina.
Lengezani kuti zimenezi zidzachitikira Yerusalemu.”
“Akazitape* akubwera kuchokera kudziko lakutali
Ndipo adzalengeza mofuula zimene zidzachitikire mizinda ya Yuda.
-