Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 8:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho ndinalowa ndipo nditayangʼana ndinaona zithunzi za zinthu zosiyanasiyana zokwawa, nyama zonyansa+ komanso mafano onse onyansa* a Aisiraeli.+ Zithunzizo zinajambulidwa pamakoma onse mochita kugoba. 11 Ndipo akuluakulu 70 a nyumba ya Isiraeli anali ataimirira patsogolo pa mafanowo. Pakati pawo panalinso Yaazaniya mwana wa Safani.+ Aliyense ananyamula chiwaya chofukizira nsembe mʼmanja mwake ndipo utsi wonunkhira wa zofukizazo unkakwera mʼmwamba.+

  • Hoseya 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Pamene iwo* ankawaitana kwambiri,

      Mʼpamenenso iwo ankawathawa kwambiri.+

      Ankapereka nsembe kwa zifaniziro za Baala,+

      Ndipo nsembezo ankaziperekanso kwa zifaniziro zogoba.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani