Yeremiya 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse omwe anali aneneri. Ankawatumiza mobwerezabwereza* koma inu simunawamvere kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+ Ezekieli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Iwe mwana wa munthu, ine ndakuika kuti ukhale mlonda wa nyumba ya Isiraeli.+ Choncho ukamva mawu ochokera pakamwa panga ukuyenera kuwachenjeza.+ Habakuku 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse omwe anali aneneri. Ankawatumiza mobwerezabwereza* koma inu simunawamvere kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+
17 “Iwe mwana wa munthu, ine ndakuika kuti ukhale mlonda wa nyumba ya Isiraeli.+ Choncho ukamva mawu ochokera pakamwa panga ukuyenera kuwachenjeza.+