-
Yesaya 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+
Iwo amagwadira ntchito ya manja awo,
Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.
-