-
Yesaya 48:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chifukwa ndinadziwa kuti ndinu anthu ouma khosi,
Kuti khosi lanu lili ngati mtsempha wachitsulo ndiponso kuti chipumi chanu chili ngati kopa,*+
-
Yeremiya 5:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma anthu awa ali ndi mtima wosamvera komanso wopanduka.
Achoka panjira yanga ndipo akuyenda mʼnjira yawo.+
-
-
-