Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Samueli 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Komanso Likasa la Mulungu linalandidwa, ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana a Eli, anaphedwa.+

  • Salimo 78:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Pamapeto pake anasiya chihema cha ku Silo,+

      Tenti imene ankakhalamo pakati pa anthu.+

  • Yeremiya 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 ine ndidzachititsa kuti nyumba iyi ikhale ngati Silo.+ Ndidzawononga mzindawu ndipo mitundu yonse yapadziko lapansi idzaugwiritsa ntchito ngati chitsanzo potemberera.’”’”+

  • Yeremiya 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Nʼchifukwa chiyani wanenera mʼdzina la Yehova kuti, ‘Nyumba iyi idzakhala ngati Silo ndipo mzinda uwu udzawonongedwa moti simudzapezeka aliyense wokhalamoʼ?” Ndiyeno anthu onse anabwera mʼnyumba ya Yehova nʼkuzungulira Yeremiya.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani