Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 22:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Nʼchifukwa chake ndanena kuti: “Musandiyangʼanitsitse,

      Ine ndilira mopwetekedwa mtima.+

      Musaumirire kunditonthoza

      Pamene ndikulira chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga.+

  • Yeremiya 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo mukakana kumvera,

      Ndidzalira mobisa chifukwa cha kunyada kwanu.

      Ndidzagwetsa misozi yambiri ndipo misozi idzatsika kuchokera mʼmaso mwanga+

      Chifukwa nkhosa za Yehova+ zagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani