Yesaya 59:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa mʼmanja mwanu mwaipitsidwa ndi magazi+Ndipo zala zanu zaipitsidwa ndi zolakwa. Milomo yanu imalankhula zabodza+ ndipo lilime lanu limanena zinthu zopanda chilungamo.
3 Chifukwa mʼmanja mwanu mwaipitsidwa ndi magazi+Ndipo zala zanu zaipitsidwa ndi zolakwa. Milomo yanu imalankhula zabodza+ ndipo lilime lanu limanena zinthu zopanda chilungamo.