Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Anthu anga ndi opusa.+Iwo saganizira za ine. Ndi ana opusa ndipo samvetsa zinthu. Amaoneka ochenjera* akamachita zoipa,Koma sadziwa kuchita zabwino.”
22 “Anthu anga ndi opusa.+Iwo saganizira za ine. Ndi ana opusa ndipo samvetsa zinthu. Amaoneka ochenjera* akamachita zoipa,Koma sadziwa kuchita zabwino.”