-
Yesaya 1:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndidzakupatsani chilango,
Ndidzakuyengani nʼkuchotseratu zonyansa zanu zonse,
Ndidzachotsa zinthu zonse zimene zikuchititsa kuti musakhale oyera.+
-