-
Yeremiya 4:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Yehova wanena kuti: “Dziko lonseli lidzakhala bwinja,+
Koma sindidzaliwonongeratu.
-
-
Yeremiya 25:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja ndipo lidzakhala chinthu chochititsa mantha. Mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+
-
-
Yeremiya 32:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Anthu adzagulanso minda mʼdziko lino,+ ngakhale mukunena kuti: “Dziko ili ndi bwinja, lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yakutchire ndipo laperekedwa kwa Akasidi.”’
-