Oweruza 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Aisiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo. Iwo ankalambiranso Abaala+ ndi mizati yopatulika.*+ 1 Samueli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Hoseya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene iwo* ankawaitana kwambiri,Mʼpamenenso iwo ankawathawa kwambiri.+ Ankapereka nsembe kwa zifaniziro za Baala,+Ndipo nsembezo ankaziperekanso kwa zifaniziro zogoba.+
7 Choncho Aisiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo. Iwo ankalambiranso Abaala+ ndi mizati yopatulika.*+
2 Pamene iwo* ankawaitana kwambiri,Mʼpamenenso iwo ankawathawa kwambiri.+ Ankapereka nsembe kwa zifaniziro za Baala,+Ndipo nsembezo ankaziperekanso kwa zifaniziro zogoba.+