-
Yeremiya 23:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wadzudzula aneneriwo kuti:
“Ndiwadyetsa chitsamba chowawa
Ndipo ndiwapatsa madzi apoizoni kuti amwe.+
Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko wafalikira mʼdziko lonse.”
-
-
Maliro 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Wandikhutitsa zinthu zowawa ndipo wandichititsa kuti ndidye chitsamba chowawa.+
-