-
Ezekieli 7:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Anthu awo amene adzapulumuke adzathawira kumapiri ndipo mofanana ndi njiwa zamʼzigwa, aliyense adzalira chifukwa cha zolakwa zake.+
-
-
Mika 1:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ndidzalira ngati mimbulu,
Ndiponso ngati nthiwatiwa.
Mliri umenewu wafalikira mpaka kukafika pageti la anthu amtundu wanga ku Yerusalemu.+
-