-
Yeremiya 25:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+
-
-
Yeremiya 49:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Ngamila zawo zidzalandidwa,
Ndipo ziweto zawo zochulukazo zidzatengedwa ndi adani.
-