Deuteronomo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 32:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti anthu a Yehova ndi gawo lake.+Yakobo ndiye cholowa chake.+ 10 Anamupeza mʼdziko lachipululu,+Mʼchipululu chopanda kanthu, molira zilombo.+ Anamuzungulira kuti amuteteze, anamusamalira,+Ndipo anamuteteza ngati mwana wa diso lake.+
9 Pakuti anthu a Yehova ndi gawo lake.+Yakobo ndiye cholowa chake.+ 10 Anamupeza mʼdziko lachipululu,+Mʼchipululu chopanda kanthu, molira zilombo.+ Anamuzungulira kuti amuteteze, anamusamalira,+Ndipo anamuteteza ngati mwana wa diso lake.+