-
Yesaya 44:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Anzake onse adzachititsidwa manyazi,+
Amisiriwo ndi anthu basi.
Onsewo asonkhane pamodzi ndipo akhale pamalo awo.
Adzachita mantha ndipo onsewo adzachititsidwa manyazi.
-