Yeremiya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iwe usawapempherere anthu awa. Usafuule kwa ine, kuwapempherera kapena kundichonderera kuti ndiwathandize,+ chifukwa ine sindidzakumvetsera.+ Yeremiya 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iwe,* usawapempherere anthu awa. Usandilirire kuti ndiwathandize kapena kuwapempherera,+ chifukwa ine sindidzamvetsera pamene iwo akundiitana chifukwa cha tsoka limene lawagwera.
16 Koma iwe usawapempherere anthu awa. Usafuule kwa ine, kuwapempherera kapena kundichonderera kuti ndiwathandize,+ chifukwa ine sindidzakumvetsera.+
14 Koma iwe,* usawapempherere anthu awa. Usandilirire kuti ndiwathandize kapena kuwapempherera,+ chifukwa ine sindidzamvetsera pamene iwo akundiitana chifukwa cha tsoka limene lawagwera.