Yeremiya 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘Mʼmizinda yamʼmadera amapiri, mʼmizinda yamʼchigwa, mʼmizinda yakumʼmwera, mʼdziko la Benjamini, mʼmadera ozungulira Yerusalemu+ ndi mʼmizinda ya Yuda,+ ziweto zidzadutsanso pansi pa dzanja la munthu amene akuziwerenga,’ akutero Yehova.”
13 ‘Mʼmizinda yamʼmadera amapiri, mʼmizinda yamʼchigwa, mʼmizinda yakumʼmwera, mʼdziko la Benjamini, mʼmadera ozungulira Yerusalemu+ ndi mʼmizinda ya Yuda,+ ziweto zidzadutsanso pansi pa dzanja la munthu amene akuziwerenga,’ akutero Yehova.”