-
Yesaya 44:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mmisiri wosema mtengo watambasula chingwe choyezera. Walemba mtengowo ndi choko chofiira.
Wausema ndi sompho* ndipo waulemberera ndi chipangizo cholembera mizere yozungulira.
-