-
Yoswa 15:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ichi chinali cholowa cha fuko la Yuda, motsatira mabanja awo.
-
-
Yoswa 15:60Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
60 Kiriyati-baala, kutanthauza Kiriyati-yearimu+ ndi Raba. Mizinda iwiri ndi midzi yake.
-
-
Yoswa 18:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kumadzulo kwa gawolo, malirewo anakhotera kumʼmwera, paphiri loyangʼanizana ndi kumʼmwera kwa Beti-horoni. Kuchokera pamenepo anakathera ku Kiriyati-baala, kutanthauza Kiriyati-yearimu,+ womwe ndi mzinda wa Yuda. Amenewa ndi malire akumadzulo a gawo la Benjamini.
-