Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 25:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Edomu wabwezera zoipa kwa nyumba ya Yuda ndipo wapalamula mlandu waukulu chifukwa chowabwezera.+ 13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Nditambasulanso dzanja langa nʼkulanga Edomu ndipo ndipha anthu ndi ziweto mʼdzikolo, moti ndidzalisandutsa bwinja.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga kuyambira ku Temani mpaka ku Dedani.+

  • Obadiya 1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Awa ndi masomphenya a Obadiya:*

      Zimene Yehova Ambuye Wamkulu Koposa akunena zokhudza Edomu+ ndi izi:

      “Ife tamva uthenga wochokera kwa Yehova,

      Ndipo nthumwi yatumidwa kwa anthu amitundu ina kukanena kuti:

      ‘Konzekani! Tiyeni tikamenyane naye.’”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani