Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Uwu ndi uthenga wokhudza Turo:+

      Lirani mofuula inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,+

      Chifukwa chakuti doko lawonongedwa ndipo simungathenso kufikapo.

      Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+

  • Yeremiya 47:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Chifukwa tsiku limene likubweralo lidzawononga Afilisiti+ onse.

      Lidzawononga aliyense wotsala amene akuthandiza Turo+ ndi Sidoni.+

      Chifukwa Yehova adzawononga Afilisiti,

      Amene ndi otsala ochokera pachilumba cha Kafitori.*+

  • Ezekieli 26:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndikuukira iwe Turo ndipo ndikutumizira mayiko ambiri kuti adzamenyane nawe. Iwo adzabwera ngati mafunde amʼnyanja.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani