Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Unatenga zovala zako zina za mitundu yosiyanasiyana nʼkukongoletsera malo okwezeka pamene unkachitirapo uhule.+ Zinthu zimene siziyenera kuchitika ndipo zisadzachitikenso.

  • Ezekieli 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ine ndinawalowetsa mʼdziko limene ndinalumbira kuti ndidzawapatsa.+ Koma ataona mapiri onse ataliatali ndi mitengo ya masamba ambiri,+ anayamba kupereka nsembe zawo ndi zopereka zawo zimene sizinkandisangalatsa. Anapereka kafungo kosangalatsa* ka nsembe zawo ndiponso kuthira nsembe zawo zachakumwa pamalo amenewo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani