Ezekieli 34:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzazipatsa mʼbusa mmodzi+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala mʼbusa wawo ndipo azidzazidyetsa.+ Ezekieli 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo+ ndipo onsewo adzakhala ndi mʼbusa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga ndiponso kusunga malamulo anga mosamala kwambiri.+ Hoseya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Aisiraeli adzabwerera nʼkuyamba kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndi Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera ndipo adzafunafuna ubwino wake mʼmasiku otsiriza.+
23 Ndidzazipatsa mʼbusa mmodzi+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala mʼbusa wawo ndipo azidzazidyetsa.+
24 Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo+ ndipo onsewo adzakhala ndi mʼbusa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga ndiponso kusunga malamulo anga mosamala kwambiri.+
5 Kenako Aisiraeli adzabwerera nʼkuyamba kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndi Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera ndipo adzafunafuna ubwino wake mʼmasiku otsiriza.+