Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 30:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yehova Mulungu wanu adzakubweretsani mʼdziko limene makolo anu analitenga kuti likhale lawo, ndipo lidzakhala lanu. Iye adzachititsa kuti zinthu zikuyendereni bwino ndipo adzakuchulukitsani kwambiri kuposa makolo anu.+

  • Yesaya 27:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mʼmasiku amene akubwerawo, Yakobo adzamera mizu,

      Isiraeli adzaphuka nʼkuchita maluwa,+

      Ndipo iwo adzadzaza dzikolo ndi zipatso.+

  • Zekariya 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 ‘Ndidzawaitana ndi likhweru nʼkuwasonkhanitsa pamodzi.

      Popeza ndidzawawombola,+ iwo adzachuluka.

      Ndipo adzapitiriza kuchuluka.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani