-
Ezara 3:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Anthu ankalephera kusiyanitsa phokoso la chisangalalo ndi la kulira, chifukwa anthu osangalalawo ankafuula kwambiri, ndipo phokoso lawo linkamveka kutali kwambiri.
-