-
Yeremiya 39:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona. Inaphanso anthu onse olemekezeka a ku Yuda.+
-