Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 38:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pakapita masiku ambiri, iwe udzaitanidwa. Ndiye pakadzapita zaka zambiri, udzalowa mʼdziko la anthu amene anabwerera kwawo. Anthu amenewa anapulumuka, lupanga litawononga dziko lawo. Kenako anasonkhanitsidwa pamodzi kuchokera kumitundu ina ya anthu nʼkukakhala kumapiri a ku Isiraeli amene anakhala ali owonongeka kwa nthawi yaitali. Anthu amene akukhala mʼdzikoli anawabwezeretsa kwawo kuchokera kwa anthu a mitundu ina. Onsewo akukhala mʼdzikoli motetezeka.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani