-
Yoweli 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Yehova adzabangula kuchokera ku Ziyoni,
Ndipo adzalankhula mokweza ali ku Yerusalemu.
Kumwamba ndi dziko lapansi zidzagwedezeka.
Koma Yehova adzakhala malo othawirako a anthu ake,+
Malo achitetezo champhamvu kwa Aisiraeli.
-