-
Yeremiya 25:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 ‘Phokoso lidzamveka kumalekezero a dziko lapansi,
Chifukwa Yehova akufuna kuimba mlandu mitundu ya anthu.
Iye adzapereka yekha chiweruzo kwa anthu onse.+
Ndipo anthu oipa adzawapha ndi lupanga,’ akutero Yehova.
-