Yeremiya 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzawapatsa mtima woti andidziwe kuti ine ndine Yehova.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ chifukwa adzabwerera kwa ine ndi mtima wawo wonse.+ Yeremiya 31:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Pangano limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili: Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,” akutero Yehova.+ Yeremiya 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ komanso kuwachititsa kuti aziyenda mʼnjira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzachita zimenezi kuti iwo limodzi ndi ana awo zinthu ziziwayendera bwino.+
7 Ndidzawapatsa mtima woti andidziwe kuti ine ndine Yehova.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ chifukwa adzabwerera kwa ine ndi mtima wawo wonse.+
33 “Pangano limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili: Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,” akutero Yehova.+
39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ komanso kuwachititsa kuti aziyenda mʼnjira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzachita zimenezi kuti iwo limodzi ndi ana awo zinthu ziziwayendera bwino.+