- 
	                        
            
            Yeremiya 22:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        18 Choncho ponena za Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, Yehova wanena kuti, ‘Sadzamulira ngati mmene anthu amachitira kuti: “Mayo ine mchimwene wanga! Mayo ine mchemwali wanga!” Sadzamulira kuti: “Mayo ine mbuye wanga! Mayo ine a mfumu aja!” 
 
-