Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 8:49, 50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 inuyo, kumwamba kumene mumakhalako,+ mumve pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo ndipo muonetsetse kuti chilungamo chachitika kwa iwo. 50 Mukhululukire anthu anu amene anakuchimwirani. Muwakhululukire zimene anakulakwirani. Muchititse kuti adani awo amene anawatenga azikhudzidwa mtima ndipo aziwamvera chisoni,+

  • Salimo 106:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Salimo 106:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Iye ankachititsa kuti anthu onse amene anawagwira ukapolo+

      Awamvere chisoni.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani