-
Danieli 4:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Koma chifukwa ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo ndi mizu yake,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndi amene akulamulira kumwamba.
-