-
Danieli 3:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Kenako Mfumu Nebukadinezara inatumiza uthenga kwa masatarapi,* akuluakulu a boma, abwanamkubwa, alangizi, asungichuma, oweruza, akuluakulu a zamalamulo ndi oyangʼanira onse a zigawo kuti asonkhane kumwambo wotsegulira fano limene Mfumu Nebukadinezara inaimika.
-