-
Esitere 8:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiye inu lembani makalata mʼmalo mwa Ayuda. Mulembe mʼdzina la mfumu zilizonse zimene mukuona kuti nʼzabwino ndipo mudinde makalatawo ndi mphete yodindira ya mfumu. Chifukwa nʼzosatheka kufafaniza lamulo limene lalembedwa mʼdzina la mfumu nʼkudindidwa ndi mphete yake yodindira.”+
-